Two arrested during Bullets and Moyale match at Kamuzu Stadium

Wa Ganyu 

On Sunday, during the FCB Nyasa Big Bullets match against Moyale Barracks at Kamuzu Stadium, police arrested a man who was selling tickets.

Surprisingly, the suspect was selling those tickets at K3 000 instead of the match day price K4 000 .

When quizzed, the suspect said someone gave him those tickets to sell. By that time, the suspect was remaining with 3 tickets. He promised the police officer: “Akatha ndikatenga ena.’

The suspect had implicated another man, that’s a person who produced those tickets. Police managed to contact that person and yes, he admitted that he gave the suspect those tickets to sell.

It was at the same time that police arrested the second suspect.

The match only grossed K18 million.

 

Chichewa:

Dzulo apolisi adanjata mkulu wina amene adamupeza akugulitsa matikiti a masewero a FCB Nyasa Big Bullets ndi Moyale Barracks mu ligi.

Pamene apolisi amatola mkuluyo mkuti atatsala ndi matikiti atatu okha koma ati adalonjeza kuti akatha akatenga ena kuti atsatse.

Iye amagulitsa tikiti imodzi K3 000 m’malo mwa K4 000 omwe udali mtengo wovomerezeka patsiku la masewero.

Woganiziridwayo atamupana adaulula kuti watumidwa ndi mkulu wina amene ati ndiye adapanga matikitiwo.

Apa apolisi adamuitana mkuluyo amene wadzavomera kutidi matikitiwo amachokera kwa iye.

Apolisi sadachedwe koma kumuvekanso chibangiri pa mmikono ndiye amutsekera m’chotokosi.

Matikitiko ndi enieni osati achinyengo. Sizikudziwika kuti zidakhala bwanji kuti matikitiko apezeke mmanja mwawo.